2 Mafumu 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Elisa anati: “Musawaphe. Kodi mukufuna kupha anthu amene mwawagonjetsa ndi lupanga ndi uta n’kuwagwira?+ Apatseni chakudya ndi madzi kuti adye ndi kumwa.+ Kenako apite kwa mbuye wawo.” Yakobo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati m’bale kapena mlongo ali waumphawi ndipo alibe chakudya chokwanira pa tsikulo,+
22 Koma Elisa anati: “Musawaphe. Kodi mukufuna kupha anthu amene mwawagonjetsa ndi lupanga ndi uta n’kuwagwira?+ Apatseni chakudya ndi madzi kuti adye ndi kumwa.+ Kenako apite kwa mbuye wawo.”