Deuteronomo 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ngati mzindawo wakupatsani yankho la mtendere ndipo akutsegulirani zipata zake, pamenepo anthu onse opezeka mmenemo azikhala anu kuti azikugwirirani ntchito yaukapolo. Iwo azikutumikirani.+
11 Ndiyeno ngati mzindawo wakupatsani yankho la mtendere ndipo akutsegulirani zipata zake, pamenepo anthu onse opezeka mmenemo azikhala anu kuti azikugwirirani ntchito yaukapolo. Iwo azikutumikirani.+