Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Ndipo akapolowa muzisiyira ana anu monga cholowa chawo mpaka kalekale.+ Amenewa ndiwo azikhala akapolo* anu, koma abale anu, ana a Isiraeli, musawapondereze ndi kuwachitira nkhanza.+

  • Deuteronomo 20:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Muzichita zimenezi ndi mizinda yonse yakutali kwambiri ndi inu imene siili pakati pa mizinda ya mitundu iyi.

  • Yoswa 9:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pambuyo pake Yoswa anaitana anthuwo, n’kuwafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani munatipusitsa ponena kuti ‘Timakhala kutali kwambiri ndi inu,’+ pamene mukukhala nafe pafupi chonchi?+

  • Yoswa 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chotero pa tsikuli, Yoswa anawaika+ kukhala otola nkhuni ndi otungira madzi Aisiraeli,+ ndiponso kuti azitola nkhuni ndi kutunga madzi a paguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena