Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Oyamba kubwerera n’kukakhala ku cholowa chawo m’mizinda yawo anali Aisiraeli,+ ansembe,+ Alevi,+ ndi Anetini.+

  • Ezara 7:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Amuna inu mudziwe kuti ansembe,+ Alevi,+ oimba,+ alonda a pakhomo,+ Anetini,+ ndi anthu ogwira ntchito panyumba ya Mulunguyi, musawakhometse msonkho umene munthu aliyense amakhoma, msonkho wakatundu,+ kapena msonkho wapanjira.+

  • Ezara 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu+ oti akauze Ido ndi abale ake Anetini+ ku Kasifiyako, kuti atibweretsere atumiki+ a panyumba ya Mulungu wathu.

  • Nehemiya 3:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.

  • Nehemiya 7:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Anetini onse+ pamodzi ndi ana a atumiki a Solomo analipo 392.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena