Yoswa 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano mukhala anthu otembereredwa.+ Mukhala akapolo+ otola nkhuni ndi otungira madzi nyumba ya Mulungu wanga ku nthawi yonse.”+ Ezara 2:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Anetini+ onse pamodzi ndi ana a atumiki a Solomo analipo 392.+ Nehemiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda. Nehemiya 7:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Anetini:+ Ana a Ziha, ana a Hasufa, ana a Tabaoti,+
23 Tsopano mukhala anthu otembereredwa.+ Mukhala akapolo+ otola nkhuni ndi otungira madzi nyumba ya Mulungu wanga ku nthawi yonse.”+
26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.