Deuteronomo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ana anu, akazi anu,+ alendo+ okhala mkati mwa msasa wanu, kuyambira wokutolerani nkhuni mpaka wokutungirani madzi,+ Ezara 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu+ oti akauze Ido ndi abale ake Anetini+ ku Kasifiyako, kuti atibweretsere atumiki+ a panyumba ya Mulungu wathu.
11 ana anu, akazi anu,+ alendo+ okhala mkati mwa msasa wanu, kuyambira wokutolerani nkhuni mpaka wokutungirani madzi,+
17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu+ oti akauze Ido ndi abale ake Anetini+ ku Kasifiyako, kuti atibweretsere atumiki+ a panyumba ya Mulungu wathu.