Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Tsopano mukhala anthu otembereredwa.+ Mukhala akapolo+ otola nkhuni ndi otungira madzi nyumba ya Mulungu wanga ku nthawi yonse.”+

  • 1 Mbiri 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Oyamba kubwerera n’kukakhala ku cholowa chawo m’mizinda yawo anali Aisiraeli,+ ansembe,+ Alevi,+ ndi Anetini.+

  • Ezara 2:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Anetini:+ Ana a Ziha, ana a Hasufa, ana a Tabaoti,+

  • Ezara 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu+ oti akauze Ido ndi abale ake Anetini+ ku Kasifiyako, kuti atibweretsere atumiki+ a panyumba ya Mulungu wathu.

  • Ezara 8:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kuchokera pa Anetini amene Davide ndi akalonga anawaika kuti azitumikira Alevi, panali Anetini 220. Onsewa anawasankha pochita kuwatchula mayina awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena