Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno atsogoleriwo anawauza kuti: “Akhale ndi moyo, ndipo akhale otola nkhuni ndi otungira madzi khamu lonse la Isiraeli,+ monga mmene tinawalonjezera.”+

  • Yoswa 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chotero pa tsikuli, Yoswa anawaika+ kukhala otola nkhuni ndi otungira madzi Aisiraeli,+ ndiponso kuti azitola nkhuni ndi kutunga madzi a paguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.

  • 1 Mbiri 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Oyamba kubwerera n’kukakhala ku cholowa chawo m’mizinda yawo anali Aisiraeli,+ ansembe,+ Alevi,+ ndi Anetini.+

  • Ezara 2:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Anetini+ onse pamodzi ndi ana a atumiki a Solomo analipo 392.+

  • Nehemiya 3:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena