Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chotero pa tsikuli, Yoswa anawaika+ kukhala otola nkhuni ndi otungira madzi Aisiraeli,+ ndiponso kuti azitola nkhuni ndi kutunga madzi a paguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.

  • Ezara 2:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Anetini:+ Ana a Ziha, ana a Hasufa, ana a Tabaoti,+

  • Ezara 8:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kuchokera pa Anetini amene Davide ndi akalonga anawaika kuti azitumikira Alevi, panali Anetini 220. Onsewa anawasankha pochita kuwatchula mayina awo.

  • Nehemiya 3:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena