Yoswa 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yoswa anagwirizana nawo za mtendere,+ ndipo anachita nawo pangano kuti asawaphe. Zitatero, atsogoleri+ a Isiraeli analumbira kwa anthuwo.+
15 Choncho Yoswa anagwirizana nawo za mtendere,+ ndipo anachita nawo pangano kuti asawaphe. Zitatero, atsogoleri+ a Isiraeli analumbira kwa anthuwo.+