Levitiko 25:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu n’kudzigulitsa kwa inu,+ musam’gwiritse ntchito ngati kapolo.+ Levitiko 25:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Musamupondereze ndi kumuchitira nkhanza,+ ndipo muziopa Mulungu wanu.+