Levitiko 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Munthu akachimwa mwa kuchita mosakhulupirika kwa Yehova+ chifukwa wanyenga+ mnzake pa chinthu chimene chili m’manja mwake, kapena chimene mnzake wam’sungitsa,+ kapena wafwamba mnzake, kapena wam’bera mwachinyengo,+
2 “Munthu akachimwa mwa kuchita mosakhulupirika kwa Yehova+ chifukwa wanyenga+ mnzake pa chinthu chimene chili m’manja mwake, kapena chimene mnzake wam’sungitsa,+ kapena wafwamba mnzake, kapena wam’bera mwachinyengo,+