Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Munthu akachita mosakhulupirika mwa kuchimwira zinthu zopatulika za Yehova+ mosadziwa, pamenepo azibweretsa kwa Yehova nkhosa yamphongo yopanda chilema kuti ikhale nsembe yake ya kupalamula.+ Nkhosayo mtengo wake uzikhala masekeli* asiliva+ ofanana ndi sekeli la kumalo oyera* kuti ikhale nsembe ya kupalamula.

  • Numeri 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Lankhula kwa ana a Isiraeli kuti, ‘Mwamuna kapena mkazi akachita machimo alionse amene anthu amachita, kuchimwira Yehova, iyenso azikhala ndi mlandu.+

  • Salimo 51:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+

      Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+

      Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+

      Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena