Deuteronomo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+ Miyambo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Wopatsa zinthu munthu wosauka sadzasowa kanthu,+ koma wophimba maso ake adzapeza matemberero ambiri.+
11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+
27 Wopatsa zinthu munthu wosauka sadzasowa kanthu,+ koma wophimba maso ake adzapeza matemberero ambiri.+