Miyambo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+ Mateyu 5:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Munthu akakupempha kanthu m’patse, ndipo munthu wofuna kukongola kanthu kwa iwe popanda chiwongoladzanja usamukanize.+ Luka 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge. Machitidwe 2:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Anali kugulitsa malo awo ndi zina zimene anali nazo,+ n’kugawa kwa onse zimene apeza, aliyense malinga ndi kusowa kwake.+
27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+
42 Munthu akakupempha kanthu m’patse, ndipo munthu wofuna kukongola kanthu kwa iwe popanda chiwongoladzanja usamukanize.+
33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge.
45 Anali kugulitsa malo awo ndi zina zimene anali nazo,+ n’kugawa kwa onse zimene apeza, aliyense malinga ndi kusowa kwake.+