Machitidwe 2:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ankagulitsa malo awo ndi zinthu zina zimene anali nazo+ nʼkugawa kwa onse zimene apeza, mogwirizana ndi zimene aliyense akufunikira.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:45 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 27 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 306/1/1990, tsa. 13
45 Ankagulitsa malo awo ndi zinthu zina zimene anali nazo+ nʼkugawa kwa onse zimene apeza, mogwirizana ndi zimene aliyense akufunikira.+