Levitiko 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ukamagulitsa malonda kwa mnzako kapena kugula zinthu kwa mnzako, musamachitirane chinyengo.+ Miyambo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu wonyoza mnzake ndiye kuti akuchimwa,+ koma wodala ndi munthu wokomera mtima anthu osautsika.+
21 Munthu wonyoza mnzake ndiye kuti akuchimwa,+ koma wodala ndi munthu wokomera mtima anthu osautsika.+