Salimo 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Wodala ndi munthu amene amachita zinthu moganizira munthu wonyozeka.+Pa tsiku la tsoka, Yehova adzamupulumutsa.+ Miyambo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Wokomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+ ndipo adzam’bwezera zimene anachitazo.+ Miyambo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Wopatsa zinthu munthu wosauka sadzasowa kanthu,+ koma wophimba maso ake adzapeza matemberero ambiri.+ Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+ Ezekieli 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ngati sazunza munthu aliyense,+ ngati amabweza chikole kwa munthu amene anakongola zinthu zake,+ ngati salanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati amapatsa munthu wanjala chakudya+ ndi kuphimba munthu wamaliseche ndi chovala,+
41 Wodala ndi munthu amene amachita zinthu moganizira munthu wonyozeka.+Pa tsiku la tsoka, Yehova adzamupulumutsa.+
27 Wopatsa zinthu munthu wosauka sadzasowa kanthu,+ koma wophimba maso ake adzapeza matemberero ambiri.+
7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+
7 ngati sazunza munthu aliyense,+ ngati amabweza chikole kwa munthu amene anakongola zinthu zake,+ ngati salanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati amapatsa munthu wanjala chakudya+ ndi kuphimba munthu wamaliseche ndi chovala,+