Yobu 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati ndinkaona munthu akuzunzika chifukwa chosowa chovala,+Kapena kuona kuti wosauka alibe chofunda, Salimo 106:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo anali kuchititsa kuti anthu onse owagwira ukapoloAwamvere chisoni.+ Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+
19 Ngati ndinkaona munthu akuzunzika chifukwa chosowa chovala,+Kapena kuona kuti wosauka alibe chofunda, Salimo 106:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo anali kuchititsa kuti anthu onse owagwira ukapoloAwamvere chisoni.+ Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+
7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+