Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Mukhululukire+ anthu anu amene anakuchimwirani.+ Muwakhululukirenso chifukwa cha malamulo anu onse amene anaphwanya,+ komanso owagwirawo akamawaona azikhudzidwa mtima+ ndi kuwachitira chisoni,

  • Ezara 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ngakhale kuti ndife akapolo,+ Mulungu wathu sanatisiye mu ukapolo wathuwo,+ koma watisonyeza kukoma mtima kosatha pamaso pa mafumu a ku Perisiya.+ Wachita zimenezi kuti atitsitsimutse n’cholinga choti tikamange nyumba ya Mulungu wathu+ komanso tikakonze malo ozungulira nyumbayo amene anali bwinja,+ ndi kuti tikhale mu Yuda ndi mu Yerusalemu ngati kuti tili mumpanda wamiyala.+

  • Yeremiya 42:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndidzakuchitirani chifundo moti mfumuyo idzakumverani chifundo ndi kukubwezerani kudziko lanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena