1 Mafumu 8:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mukhululukire anthu anu amene anakuchimwirani. Muwakhululukire zimene anakulakwirani. Muchititse kuti adani awo amene anawatenga azikhudzidwa mtima ndipo aziwamvera chisoni,+
50 Mukhululukire anthu anu amene anakuchimwirani. Muwakhululukire zimene anakulakwirani. Muchititse kuti adani awo amene anawatenga azikhudzidwa mtima ndipo aziwamvera chisoni,+