Salimo 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musakumbukire machimo a pa unyamata wanga ndi zolakwa zanga.+Ndikumbukireni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ubwino wanu, inu Yehova.+ Maliko 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndithu ndikukuuzani, ana a anthu adzakhululukidwa zinthu zonse, kaya ndi machimo otani amene anachita kapena mawu onyoza otani amene analankhula.+ Luka 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 [[Koma Yesu anati: “Atate, akhululukireni,+ chifukwa sakudziwa chimene akuchita.”]]* Ndipo iwo anagawana malaya ake mwa kuchita maere.+
7 Musakumbukire machimo a pa unyamata wanga ndi zolakwa zanga.+Ndikumbukireni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ubwino wanu, inu Yehova.+
28 Ndithu ndikukuuzani, ana a anthu adzakhululukidwa zinthu zonse, kaya ndi machimo otani amene anachita kapena mawu onyoza otani amene analankhula.+
34 [[Koma Yesu anati: “Atate, akhululukireni,+ chifukwa sakudziwa chimene akuchita.”]]* Ndipo iwo anagawana malaya ake mwa kuchita maere.+