Salimo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bwererani+ mudzapulumutse moyo wanga, inu Yehova.+Ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha.+ Salimo 51:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+Malinga ndi kuchuluka kwa chifundo chanu, fafanizani zolakwa zanga.+
4 Bwererani+ mudzapulumutse moyo wanga, inu Yehova.+Ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha.+
51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+Malinga ndi kuchuluka kwa chifundo chanu, fafanizani zolakwa zanga.+