Salimo 39:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndilanditseni ku zolakwa zanga zonse.+Musalole kuti munthu wopusa azinditonza.+ Salimo 103:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Monga mmene bambo amasonyezera chifundo kwa ana ake,+Yehova wasonyezanso chifundo kwa onse omuopa.+ Miyambo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+ Yesaya 43:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ineyo ndi amene ndikufafaniza+ zolakwa zako,+ ndipo machimo ako sindidzawakumbukiranso.+ Yesaya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ngati kuti ndaziphimba ndi mtambo,+ ndi machimo ako ngati kuti ndawaphimba ndi mitambo yambiri. Bwerera kwa ine,+ ndipo ine ndikuwombola.+
13 Monga mmene bambo amasonyezera chifundo kwa ana ake,+Yehova wasonyezanso chifundo kwa onse omuopa.+
13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+
22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ngati kuti ndaziphimba ndi mtambo,+ ndi machimo ako ngati kuti ndawaphimba ndi mitambo yambiri. Bwerera kwa ine,+ ndipo ine ndikuwombola.+