Salimo 78:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma anawamvera chifundo.+ Anali kukhululukira* machimo awo+ ndipo sanali kuwawononga.+Nthawi zambiri anali kubweza mkwiyo wake,+Ndipo sanali kuwasonyeza ukali wake wonse. Yakobo 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pemphero lachikhulupiriro lidzachiritsa wodwalayo,+ ndipo Yehova adzamulimbitsa.+ Ndiponso ngati anachita machimo, adzakhululukidwa.+
38 Koma anawamvera chifundo.+ Anali kukhululukira* machimo awo+ ndipo sanali kuwawononga.+Nthawi zambiri anali kubweza mkwiyo wake,+Ndipo sanali kuwasonyeza ukali wake wonse.
15 Pemphero lachikhulupiriro lidzachiritsa wodwalayo,+ ndipo Yehova adzamulimbitsa.+ Ndiponso ngati anachita machimo, adzakhululukidwa.+