Salimo 65:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zolakwa zanga zandikulira.+Inu mudzatikhululukira* machimo athu.+ Salimo 79:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+
9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+