Salimo 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti masoka anandizungulira moti sindinathe kuwawerenga.+Zolakwa zanga zochuluka zinandifikira modzidzimutsa moti sindinathe kuziona mmene zinachulukira.+Zinachuluka kwambiri kuposa tsitsi la kumutu kwanga,+Ndipo ndinataya mtima.+ Aroma 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 koma ndimaona chilamulo china m’ziwalo zanga+ chikumenyana+ ndi chilamulo cha m’maganizo mwanga+ n’kundipanga kukhala kapolo wa chilamulo cha uchimo+ chimene chili m’ziwalo zanga. Agalatiya 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti zilakolako za thupi zimalimbana ndi mzimu,+ mzimunso umalimbana ndi thupi. Zinthu ziwiri zimenezi zimatsutsana, choncho zinthu zimene mumafuna kuchita simuzichita.+
12 Pakuti masoka anandizungulira moti sindinathe kuwawerenga.+Zolakwa zanga zochuluka zinandifikira modzidzimutsa moti sindinathe kuziona mmene zinachulukira.+Zinachuluka kwambiri kuposa tsitsi la kumutu kwanga,+Ndipo ndinataya mtima.+
23 koma ndimaona chilamulo china m’ziwalo zanga+ chikumenyana+ ndi chilamulo cha m’maganizo mwanga+ n’kundipanga kukhala kapolo wa chilamulo cha uchimo+ chimene chili m’ziwalo zanga.
17 Pakuti zilakolako za thupi zimalimbana ndi mzimu,+ mzimunso umalimbana ndi thupi. Zinthu ziwiri zimenezi zimatsutsana, choncho zinthu zimene mumafuna kuchita simuzichita.+