Salimo 78:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma ankawamvera chifundo.+Ankawakhululukira* machimo awo ndipo sankawawononga.+ Nthawi zambiri ankabweza mkwiyo wake+Mʼmalo moonetsa ukali wake wonse.
38 Koma ankawamvera chifundo.+Ankawakhululukira* machimo awo ndipo sankawawononga.+ Nthawi zambiri ankabweza mkwiyo wake+Mʼmalo moonetsa ukali wake wonse.