Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+ Numeri 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Yehova ndi wosakwiya msanga, ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka.*+ Amakhululukira zolakwa ndi machimo, koma sadzalekerera wolakwa osamupatsa chilango. Amalanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.’+ Nehemiya 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndipo chifukwa cha chifundo chanu chachikulu simunawafafanize+ kapena kuwasiya, popeza ndinu Mulungu wachisomo ndi wachifundo.+
6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+
18 ‘Yehova ndi wosakwiya msanga, ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka.*+ Amakhululukira zolakwa ndi machimo, koma sadzalekerera wolakwa osamupatsa chilango. Amalanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.’+
31 Ndipo chifukwa cha chifundo chanu chachikulu simunawafafanize+ kapena kuwasiya, popeza ndinu Mulungu wachisomo ndi wachifundo.+