Afilipi 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 chifukwa ndikudziwa kuti mwa mapembedzero+ anu, ndi mwa mzimu wa Yesu Khristu,+ ndidzamasulidwa.