Yohane 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Akadzafika mthandizi amene ndidzamutumiza kuchokera kwa Atate,+ amene ndi mzimu wa choonadi wochokera kwa Atate, ameneyo adzandichitira umboni,+ 1 Petulo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anali kufufuza nyengo+ yake kapena mtundu wa nyengo imene mzimu+ umene unali mwa iwo unali kuwasonyeza yokhudzana ndi Khristu.+ Mzimuwo unali kuchitira umboni za masautso a Khristu+ ndi za ulemerero+ wobwera pambuyo pake.
26 Akadzafika mthandizi amene ndidzamutumiza kuchokera kwa Atate,+ amene ndi mzimu wa choonadi wochokera kwa Atate, ameneyo adzandichitira umboni,+
11 Anali kufufuza nyengo+ yake kapena mtundu wa nyengo imene mzimu+ umene unali mwa iwo unali kuwasonyeza yokhudzana ndi Khristu.+ Mzimuwo unali kuchitira umboni za masautso a Khristu+ ndi za ulemerero+ wobwera pambuyo pake.