Luka 24:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndipo ine ndidzatumiza kwa inu chimene Atate wanga analonjeza. Koma inu mukhalebe mumzindawu kufikira mutalandira mphamvu zochokera kumwamba.”+ Yohane 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+
49 Ndipo ine ndidzatumiza kwa inu chimene Atate wanga analonjeza. Koma inu mukhalebe mumzindawu kufikira mutalandira mphamvu zochokera kumwamba.”+
26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+