Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pambuyo pake, iwo anamva mawu a Yehova Mulungu pamene iye anali kuyendayenda m’mundamo pa nthawi ya kamphepo kayeziyezi.+ Mwamuna ndi mkaziyo atamva, anathawa n’kukabisala pakati pa mitengo ya m’mundamo kuti Yehova Mulungu asawaone.+

  • 1 Samueli 15:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Poyankha Sauli anati: “Anthuwa+ azitenga kwa Aamaleki, chifukwa sanaphe nkhosa ndi ng’ombe zabwino kwambirizi n’cholinga chofuna kuzipereka nsembe kwa Yehova Mulungu wanu.+ Koma zina zonse zotsala taziwononga.”

  • Salimo 32:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pamene ndinakhala chete osaulula machimo anga, mafupa anga anafooka, chifukwa tsiku lonse ndinali kuvutika mumtima mwanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena