Deuteronomo 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi anthu ena anamvapo mawu a Mulungu akumveka kuchokera pakati pa moto ngati mmene inuyo munawamvera, ndi kukhalabe ndi moyo?+ Deuteronomo 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu kuti akulanditseni+ ndi kupereka adani anu m’manja mwanu.+ Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu ndi kutembenuka n’kuleka kuyenda nanu limodzi.+ Machitidwe 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano Mose ataona zimenezi, anadabwa kwambiri.+ Koma pamene anali kuyandikira kuti aonetsetse, panatuluka mawu a Yehova* akuti,
33 Kodi anthu ena anamvapo mawu a Mulungu akumveka kuchokera pakati pa moto ngati mmene inuyo munawamvera, ndi kukhalabe ndi moyo?+
14 Pakuti Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu kuti akulanditseni+ ndi kupereka adani anu m’manja mwanu.+ Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu ndi kutembenuka n’kuleka kuyenda nanu limodzi.+
31 Tsopano Mose ataona zimenezi, anadabwa kwambiri.+ Koma pamene anali kuyandikira kuti aonetsetse, panatuluka mawu a Yehova* akuti,