Salimo 79:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+ Yeremiya 31:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena m’bale wake+ kuti, ‘Mum’dziwe Yehova!’+ pakuti aliyense wa iwo adzandidziwa, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu,”+ watero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+ Aheberi 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 pambuyo pake ukunenanso kuti: “Ndipo sindidzakumbukiranso machimo awo komanso zochita zawo zosonyeza kusamvera malamulo.”+
8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+
34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena m’bale wake+ kuti, ‘Mum’dziwe Yehova!’+ pakuti aliyense wa iwo adzandidziwa, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu,”+ watero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+
17 pambuyo pake ukunenanso kuti: “Ndipo sindidzakumbukiranso machimo awo komanso zochita zawo zosonyeza kusamvera malamulo.”+