Deuteronomo 28:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+ Salimo 142:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+
43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+
6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+