Salimo 143:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndisungenibe wamoyo+ chifukwa cha dzina lanu.+Chotsani moyo wanga m’masautso+ monga mwa chilungamo chanu.+
11 Inu Yehova, ndisungenibe wamoyo+ chifukwa cha dzina lanu.+Chotsani moyo wanga m’masautso+ monga mwa chilungamo chanu.+