Salimo 119:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Moyo wanga wamamatira kufumbi.+Ndisungeni wamoyo mogwirizana ndi mawu anu.+