Salimo 116:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amateteza anthu osadziwa zambiri.+Ndinali wosautsika koma iye anandipulumutsa.+