Salimo 79:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+ Salimo 106:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi zambiri anali kuwalanditsa,+Koma iwo anali kumupandukira chifukwa sanali kumumvera,+Ndipo anali kuwatsitsa chifukwa cha zolakwa zawo.+ Salimo 142:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+
8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+
43 Nthawi zambiri anali kuwalanditsa,+Koma iwo anali kumupandukira chifukwa sanali kumumvera,+Ndipo anali kuwatsitsa chifukwa cha zolakwa zawo.+
6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+