Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+ Salimo 69:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo ine mtumiki wanu musandibisire nkhope yanu.+Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndasautsika kwambiri.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+
6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+
17 Ndipo ine mtumiki wanu musandibisire nkhope yanu.+Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndasautsika kwambiri.+
22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+