Salimo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikomereni mtima inu Yehova, pakuti ndasautsika kwambiri.+Diso langa lafooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso moyo wanga ndi m’mimba mwanga.+ Salimo 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Khalani wofunitsitsa kundilanditsa, inu Yehova.+Inu Yehova, fulumirani kundithandiza.+ Salimo 70:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Inu Mulungu, fulumirani kundilanditsa,+Inu Yehova, fulumirani kundithandiza.+
9 Ndikomereni mtima inu Yehova, pakuti ndasautsika kwambiri.+Diso langa lafooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso moyo wanga ndi m’mimba mwanga.+