Salimo 38:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Fulumirani kundithandiza,+Inu Yehova, chipulumutso changa.+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 70:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Inu Mulungu, fulumirani kundilanditsa,+Inu Yehova, fulumirani kundithandiza.+