Oweruza 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ehudi atamwalira, ana a Isiraeli anayambanso kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Oweruza 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+ Ezekieli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ndikukutumiza kwa ana a Isiraeli,+ kwa mitundu yopanduka imene yandipandukira.+ Iwo ndi makolo awo akhala akuphwanya malamulo anga mpaka lero.+
8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+
3 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ndikukutumiza kwa ana a Isiraeli,+ kwa mitundu yopanduka imene yandipandukira.+ Iwo ndi makolo awo akhala akuphwanya malamulo anga mpaka lero.+