Deuteronomo 32:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anayamba kuputa nsanje+ yake ndi milungu yachilendo.+Anapitiriza kumukhumudwitsa ndi zinthu zonyansa.+ Oweruza 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo,+ n’kuyamba kutsatira milungu ina mwa milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milungu imeneyo, moti anakhumudwitsa Yehova.+ Oweruza 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ehudi atamwalira, ana a Isiraeli anayambanso kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+
16 Anayamba kuputa nsanje+ yake ndi milungu yachilendo.+Anapitiriza kumukhumudwitsa ndi zinthu zonyansa.+
12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo,+ n’kuyamba kutsatira milungu ina mwa milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milungu imeneyo, moti anakhumudwitsa Yehova.+