1 Mafumu 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ayuda anapitiriza kuchita zoipa m’maso mwa Yehova,+ moti anamuchititsa+ nsanje kuposa mmene makolo awo anamuchititsira nsanje ndi machimo awo onse amene makolowo anachita.+ 1 Akorinto 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kapena “kodi tikufuna kuputa nsanje+ ya Yehova”? Kodi mphamvu zathu zingafanane ndi zake?+
22 Ayuda anapitiriza kuchita zoipa m’maso mwa Yehova,+ moti anamuchititsa+ nsanje kuposa mmene makolo awo anamuchititsira nsanje ndi machimo awo onse amene makolowo anachita.+