Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero ana a Isiraeli anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo,+ moti anayamba kutumikira Abaala+ ndi mizati yopatulika.+

  • 2 Mafumu 17:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Komabe, nawonso Ayudawo sanasunge malamulo a Yehova Mulungu+ wawo, koma anayenda motsatira malamulo amene Aisiraeli+ anapanga.

  • 2 Mbiri 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ufumu wa Rehobowamu utangokhazikika+ ndiponso iye atangokhala wamphamvu, iye ndi Aisiraeli onse+ anasiya chilamulo cha Yehova.+

  • Yeremiya 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Nditaona zimenezo, ndinam’pitikitsa+ ndipo ndinamupatsa kalata yotsimikizira kuti ukwati watha+ chifukwa chakuti Isiraeli wosakhulupirikayu anachita chigololo. Koma Yuda amene ndi m’bale wake wochita zachinyengo sanachite mantha ndipo nayenso anayamba kuchita uhule.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena