Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati yawo yopatulika mukaidule.+

  • Deuteronomo 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+

  • Deuteronomo 16:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Usabzale mtengo wa mtundu uliwonse kuti ukhale mzati woti uziulambira pafupi ndi guwa lansembe la Yehova Mulungu wako limene udzadzipangira.+

  • 1 Mafumu 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena