Ekisodo 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati yawo yopatulika mukaidule.+ 2 Mafumu 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako anatulutsa zipilala zopatulika+ za m’kachisi wa Baala n’kuzitentha+ zonse. 2 Mafumu 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 (Koma sanasiye tchimo la nyumba ya Yerobowamu limene anachimwitsa nalo Isiraeli.+ Anayenda m’tchimolo,+ ndipo mzati wopatulika+ unali ulipobe ku Samariya.)
13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati yawo yopatulika mukaidule.+
6 (Koma sanasiye tchimo la nyumba ya Yerobowamu limene anachimwitsa nalo Isiraeli.+ Anayenda m’tchimolo,+ ndipo mzati wopatulika+ unali ulipobe ku Samariya.)