2 Mafumu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kungoti iye sanasiye kutsatira machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+ Machimo ake anali kulambira ana a ng’ombe agolide.+ Mmodzi wa ana a ng’ombe agolidewo anali ku Beteli, ndipo wina ku Dani.+ 2 Mafumu 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anang’amba Isiraeli kumuchotsa kunyumba ya Davide ndipo iwo analonga ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasiyitsa Aisiraeli kutsatira Yehova n’kuwachimwitsa ndi tchimo lalikulu.+
29 Kungoti iye sanasiye kutsatira machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+ Machimo ake anali kulambira ana a ng’ombe agolide.+ Mmodzi wa ana a ng’ombe agolidewo anali ku Beteli, ndipo wina ku Dani.+
21 Anang’amba Isiraeli kumuchotsa kunyumba ya Davide ndipo iwo analonga ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasiyitsa Aisiraeli kutsatira Yehova n’kuwachimwitsa ndi tchimo lalikulu.+